Fajr 04:42 Dhuhr 11:38 Asr 14:55 Maghrib 17:24 Isha 18:42
Blantyre, Malawi · Sunday, 1 November 2026
News October 20, 2026 By MAM Communications 33 views

Kalata Yabodza

Bungwe la Muslim Association of Malawi (MAM) lalangiza Amalawi kuti asayitengere kalata yomwe ikuzungulira pa masamba a mchezo yonena kuti bungweli lalakhulapo pa nkhani yokhudza ndale.

Bungwe la Muslim Association of Malawi (MAM) lalangiza Amalawi kuti asayitengere kalata yomwe ikuzungulira pa masamba a mchezo yonena kuti bungweli lalakhulapo pa nkhani yokhudza ndale. 

 

Mlembi wamkulu wa bungweli Alhajj Dr Twaibu Lawe ati kalatayo yalembedwa ndi anthu ena ofuna kubweretsa chisokonezo komanso kukwaniritsa zolinga zawo. 

 

Iwo apempha anthu kuti apewe kufalitsa nkhani za bodza zomwe zili nkuthekera kobweretsa mpungwepungwe mdziko muno. 

 

Kotero Mlembiyu  wapempha Atolankhani kuti aziyamba afufuza Kaye asanalembe nkhani zawo.